Kaswili MW

Kaswili MW Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Kaswili MW, Shopping & retail, kaswilimw@gmail. com, Blantyre.

29/08/2026

ndangoika popanda chifukwa

Apolice ku Zambia amanga nkulu wina chifukwa chopha nkango Koma zowona zake nkuluyu anapha chilombochi pogwilisa ntchito...
28/08/2026

Apolice ku Zambia amanga nkulu wina chifukwa chopha nkango Koma zowona zake nkuluyu anapha chilombochi pogwilisa ntchito manja ake popanda chida chilichose momwe mukuoneramu nkuluyu wavulala kwambili koma tikunena pano ali m'manja mwa police

28/08/2026

anawapelelera akuchita kusaweruzika nde anawauza kuti apitilize zisakuphonyeni 👇👇👇👇

27/08/2026

zochosa nkhawa izi ��

Apolisi m’boma la Ntcheu amanga a Simon Jalon, azaka 22, ndi a Pilirani Chabwera, azaka 31, powaganizira kuti amagulitsa...
25/08/2026

Apolisi m’boma la Ntcheu amanga a Simon Jalon, azaka 22, ndi a Pilirani Chabwera, azaka 31, powaganizira kuti amagulitsa pangolin pa mtengo wa K30 miliyoni.

Mneneri wa apolisi ku Ntcheu, a Jacob Khembo, ati awiriwa anawagwira ku Tsangano pomwe apolisi, mogwirizana ndi akuluakulu a za nkhalango, anawapeza akugulitsa pangoliniyo, anthu akufuna kwabwino atawatsina khutu.

A Khembo ati apolisi anakwanitsa kulanda pangolinuyo kwa awiriwa, ndipo panthawiyo nkuti atamuika m’thumba.

Awiriwa akuyembekezeka kukaonekera ku bwalo lamilandu posachedwapa, komwe akayankhe mlandu wopezeka ndi pangolin komanso kugulitsa nyama yotetezedwayi, zomwe ndi kuphwanya malamulo.

Wolemba Bertha Banda

mpaka zafika apa 🤣🤣🤣 zoziyamba dara izi
24/08/2026

mpaka zafika apa 🤣🤣🤣 zoziyamba dara izi

kunja kukacha kuchuluka zomvaimva nanga uwu ndiulemu 🤣🤣 ena akuti temwa ngosarakwa
24/08/2026

kunja kukacha kuchuluka zomvaimva nanga uwu ndiulemu 🤣🤣 ena akuti temwa ngosarakwa

22/08/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Mark Jameson, Mable Chikaonda, Brighton Chsnda, Andrea Zimba, Lucky Muleya, Patience Banda, Chawa Mhone, Chikondi Jimu, Adamson Dobah, Brian Edward, Eric Kumsika, Noxy Thoxy

tinene kuti ndi ntendere wampanikiza munthuyi kapena mavuto
19/08/2026

tinene kuti ndi ntendere wampanikiza munthuyi kapena mavuto

Address

Kaswilimw@gmail. Com
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kaswili MW posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share