29/07/2024
Ambuye anakonda m'mtima mwanumo kuti ndimalo abwino amene iye angakhala, choncho ndikupempani abale okondedwa kuti mukoze mitima yanu ndikumulola ambuye alamulire, akhale mbuye ndimpulumusi wamoyo wanu
May God bless you
Amen