M j kampango electronics & dish installation

M j  kampango  electronics & dish installation Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from M j kampango electronics & dish installation, Shopping & retail, Blantyre chileka, Chileka.

Ndikodoreni  ndibwere zaku ngwiriren ntchito kwanukonko olo musaza ndilipire bola muzangondi panga  zikomo  sindizadanda...
12/09/2026

Ndikodoreni ndibwere zaku ngwiriren ntchito kwanukonko olo musaza ndilipire bola muzangondi panga zikomo sindizadandaura makhara kuti ndili bwino bwino ine 🤣🤣🤣💡👷👍👍🤝

03/09/2026
✅ DoNE 👍🤝
03/09/2026

✅ DoNE 👍🤝

Ngati mumaligalira za aka👇 kumakadyera ma plan oti  mukagure kumakasungera  ndalama  kulikufunisitsa kuti   mukatenge ba...
26/08/2026

Ngati mumaligalira za aka👇 kumakadyera ma plan oti mukagure kumakasungera ndalama kulikufunisitsa kuti mukatenge basi

kameneka kapita ❌

kagulidwa ❌

muli ndi katundu woti mukufuna kuti mugulise kapena kugura komaso mulindi katundu woti anawonogeka mukusakasaka technici...
21/08/2026

muli ndi katundu woti mukufuna kuti mugulise kapena kugura komaso mulindi katundu woti anawonogeka mukusakasaka technician👷💡 musachite kupita kutali ndi kodoreni ine pono chilichonse zapanga khawa njee🤝

bwerani muzatenge katundu wabwino kwambiri ameneyi  mukampase nyamata azikubwereserani cash tsiku lina lililose kulidza ...
21/08/2026

bwerani muzatenge katundu wabwino kwambiri ameneyi mukampase nyamata azikubwereserani cash tsiku lina lililose kulidza kumapita kapena muntha kumakwera nokha timawurendo kumafupikako

price 700k

blantyre chileka

0990736368 / 088 65 56 550

kwacha tikanthamange🏃
28/07/2026

kwacha tikanthamange🏃

katundu wanu wapsa ndi moto🔥wa magesi💡 kapena wangosiya enkha enkha kungwira ntchito   ndiye mukusaka saka  munthu oti a...
04/07/2026

katundu wanu wapsa ndi moto🔥wa magesi💡 kapena wangosiya enkha enkha kungwira ntchito ndiye mukusaka saka munthu oti akukonzereni tilipo ife akaswiri pankhani yokonza konza yii!!!
timathana ndimamvuto ngati awa👇👇

PLASM Tv📺
IRON
kETTl
MICROWAVE
DVD PLAY
COOKER
HOTPLAT .....
Home gadgets and 📡 dish installation

tikupenzekera ku blantyre chileka

0990736368/ 0886556550

25/06/2026

tandiponyereni katund amene mukugulitsayo ngati mukufuna ndalama mwachangu kwambiri

anthuwa pano ali ndalama akufuna kugura akatundu osiyana siyana panja monthend musayiware 🦺🤝

Address

Blantyre Chileka
Chileka
CHANTHA

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when M j kampango electronics & dish installation posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share