04/09/2026
Sunday lapitali mwambo ULI nkati wina anaganiza zoyendera KACHISI yense, koma zomwe anapeza zinali zokhudza kwambili 😭👇
👨👩👧👦 Anthu: 400
📖 Bibles: 27
📱 Phones: 507 😭😂
🔦 Matochi otchaja: 176
💡 Nyali zotchaja: 212
🔋Ma Power banks: 432
Tadikiran… 😂😂
Nde sitinene kuti timanyamura ma power bank ochuluka kusiyana Nd ma baibulo popita Ku tchalitchi? 😭🔋📖
Ambili amabwera kuzatchaja mafoni, ena ma tochi ena kuzatchaja Nyali, … koma chosecho spiritual battery lakhara likuwonetsa 1% since 2009 😭😂
📱 Last Seen:
WhatsApp — 1 minute ago 🙃
Facebook — 2 minutes ago ☺️
Instagram — 10 minutes ago 😉
Bible — Since 2009 🙈📖😭
Panthawi iyi, Mulungu akuyang'ana Kwa anthu nkuzati:
“Mwana wanga, … inetu ndakhara online kuchokera pachiyambi ?” komano sumandiwona 😭😂🙏
Zowona zake ambili mwa Ife timaloga 5 hours osasidza, koma kungofika nthawi yowerenga Bible Kwa 5 minutes yokha, …
🥱 “Odini ndipumuzeko maso pang'ono.”
Next thing… bastu mpaka mawa mmawa 😭😂
Koma tochi yanu mumakatchaja Ku church mmayiyikira nzelutu kusiyana Nd mzimu wanu😭🔦😂
Macheza Ali apo❤️🙏
Tatengani phindi imodz yokha kumuthokoza mulungu kamba Ka mphatso yamoyo.
Kukamba zowona, sitili opambana kwa omwe agonekedwa muzipatara KT mawa aliwoneso.
Sitili opambana Kwa omwe achoka mmakwawo koma sanabwerereso.
Ndipo sindife opambana Nd akubanja omwe aluza mubare wawo lelo zosayembekezereka 💔
Chilungamo chot ULI moyo
Ukuyenda🚶
Ukudya 🍛
Kuseka 😂
Kugona mwantendere 😴
Ukugwilitsa ntchito phone yako 📱
And ukuwerenga uthengawu
…Ndichinthutu chopambana kumuthokoza mulungu. 🙏❤️
Tsku Lina battery la foniyo lizatheratu 🔋
Network siyizabweraposo 📶
Power bank siyizatchajidwa 😭
NEPA will take light 😂
Koma chifundo cha mulungu sichimasuntha ❤️🙏
Monga mukupitilza kuwerenga , posting, kucheza, kuwona ma status ndkudina foni ngat mawa kulibeso 😭😂…
Kumbukiran mulungu yemwe amakutetezani kuzoypa smunamuwonepo.
Mwakanthaw kochepa thokozan mulungu🤝