AFASA investment

AFASA  investment Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from AFASA investment, Shopping & retail, Mtsiliza, Lilongwe.

New Chimbaka voices
18/07/2026

New Chimbaka voices

Enjoy the videos and music you love, upload original content, and share it all with friends, family, and the world on YouTube.

Rest well Legend ๐Ÿ˜ฅ๐Ÿ˜ฅ๐Ÿ˜ฅ๐Ÿ˜ฅ
19/06/2026

Rest well Legend ๐Ÿ˜ฅ๐Ÿ˜ฅ๐Ÿ˜ฅ๐Ÿ˜ฅ

19/06/2026
TATHYOKA ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ’”๐Ÿ’”๐Ÿ’”.Oimba Emmanuel kambanje (Amanzy) amene anatchuka ndi nyimbo yakuti: โ€œAli busy ku delete number kuti andi...
17/06/2026

TATHYOKA ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ’”๐Ÿ’”๐Ÿ’”.

Oimba Emmanuel kambanje (Amanzy) amene anatchuka ndi nyimbo yakuti:
โ€œAli busy ku delete number kuti andiyiware.......
Koma waiwara maloto sangโ€™amba.......โ€ Watisiya lero atadwala kwa kathawi kochepa.

Emmanuel Kambanje amene amadziwika ndi dzina lakuti โ€œA Manzy,โ€ Pachifukwa cha hit song yake yotchedwa, โ€œMaloto Sangโ€™amba,โ€ muzaka zapakati pa 2019/20...,amachokera ku Zingwangwa mumzinda wa Blantyre...

MHSRIP ๐Ÿ•Š๏ธ

17/06/2026

Bwanji tingotolera ma bus amipingomu kuti akatenge amalawi ku South Africa

usadzamutole katundu uyu amatha kukuonetsa nyenyezi dzuwa likuwala
17/06/2026

usadzamutole katundu uyu amatha kukuonetsa nyenyezi dzuwa likuwala

Sad News ๐Ÿ’”๐Ÿ˜ญ Pajo Pajo mnyamata yemwe amaphunzitsa The Great Angels Choir zamavinidwe ndipo anavina nawonso munyimbo ya N...
16/06/2026

Sad News ๐Ÿ’”๐Ÿ˜ญ

Pajo Pajo mnyamata yemwe amaphunzitsa The Great Angels Choir zamavinidwe ndipo anavina nawonso munyimbo ya Nza Yahweh wamwalira. Ambuye mulandire mzimu wa Pajo๐Ÿ˜ญ MHSRIP๐Ÿ™

angakhale aboma lanji awa?
16/06/2026

angakhale aboma lanji awa?

16/06/2026

Actor

Address

Mtsiliza
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when AFASA investment posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share