07/03/2025
Nkhuku zako zamazila zikafika week 19 ngati ufuna York yake ija ikhale yellow kwambiri yokopa anthu Ku feed kuja uikeko PAPRIKA 150 grams Ku thumba la 50 Kgs.
Zija amalemba mushop michere yake ija yopangisa YellowYork Dzina lija amalemba ndilabodza amangokuphimbani kuti musaziwe amalawi ndi Paprika .
Just add paprika 150 grams Ur good