28/06/2021
PHUNZIRANI NDIKUPEZA NTCHITO ZA BAKING AND CONFECTIONERY ( MZUZU)
� Kuli maphunziro kwaanthu 20 okha azabaking komanzo zamalonda motere.
Zophunzira:
� kupanga mabanzi
� kupanga doughnuts
� kupanga Cake
� Sweet rolls
� Budget & profits for confectionery centre business
� Business Branding and Marketing.
PHINDU
1. Kupasidwa zipangizo zoyambira business (Mafuta Ophikira and Bread Flour)
2. Mwayi wa ntchito
3. Certificate of attendance
Opening Date
� 17 July, 2021
Malo: st Andrews CCAP primary, Mzuzu.
Kuti kulembesa
� M***a kubwera loweruka and Sunday lililonse Ku CCAP primary in std7 block 8:00am to 11:00am
� Or kuzalembesa Ku Mzuzu University poimba lamya pa +265(0)994598279
� Or Zalembeseni Ku Ekwendeni poimba phone pa +265(0)885890287
Fees
� Kulembesa posaina form ndi k1500
� Fees yamaphunziro ndi k15000.
Maphunzirowa apangidwa sponsor ndi Nyasa Voice Education Centre & Nyasa Investment.
Mouthpiece for youth empowerment