07/08/2025
Tiyambe ndikunena kuti ife timagula zinthu zoti zimapezeka ndipo pamitengo yathu ndiye ngati simusangalasidwai sitiumiliza munthu ayi katundu ndi wanu.
Katundu yemwe tikufuna padakali pano ndi uyu
*Ma one kwacha olembedwa 10 shillings a D.E Thomson or Allan Pereni mtengo ndi 35--40 pin each
*Ma 5 shillings a pepala mtengo ndi 35--40 pin each
*Ma One Pound a pepala a green ya Kamuzu mtengo ndi 10,000 each
*Ma 2 kwacha a green a kamuzu mtengo ndi 8,000 each
*Ma One kwacha a John Tembo a fodya mtengo ndi 5,000 each
*Ma 50 tambala a chichiri Arch mtengo ndi 5,000 each
*Ma 50 tambala a nyamata akudula mzimbe ilipamulu 6,000 each
* 5 kwacha yofiila ya John Tembo mtengo ndi 6,000 each
*Ma 10 kwacha a Phiri la Mulanje a D.E Thomson 30,000--35,000 each
*Ma 10 kwacha a phiri la mulanje a John Tembo mtengo ndi 15,000 each
*Ma British pounds coins a Elizabeth mtengo ndi 6,000 each
*Ma 200 kwacha a Bakili Muluzi mtengo ndi 4,000 each
*Ma 500 kwacha a John Chilebwe mtengo ndi 3,000 each
*Ma 100 kwacha a Maize Sailors mtengo ndi 4,000 each
*Ma two shillings a coins from 1900 to 1940 mtengo ndi 7,000 each
*Ma One shillings a coins from 1900 to 1940 mtengo ndi 7,000 each
*Ma coins a tickey or tiki ya ntunfu wina ulionseo from 1900 to 1940 mtengo ndi 5,000 each
* Ma sixpence coins from 1900 to 1940 mtengo ndi 4,000 each
*Ma florin British or half crown from 1900 to 1940 mtengo ndi 4,000 each
mitengoi ndiyomwe timagulila ifeyo bas ngati musangalasidwe inbox bas.
Timagulaso ndalama za maiko inse akuja from 1700 malile 1940 kupatula penny iliyonse
#
Zikomo\kwambili\nonse