UNDER the Mlombwa TREE

UNDER the Mlombwa TREE Very Response

29/09/2023

Hello

16/10/2019

"GOLIDE " motsatana ndi "NTHAWI "

Izi ndi nkhani zimene zikubweleranso m'bwalo ...

Ndine Admin wanu (left in full blue work-suit)Ma busy achepa tsopano, ndikhala ndikupitiliza nkhani zonse mwanthawi imod...
20/02/2018

Ndine Admin wanu (left in full blue work-suit)
Ma busy achepa tsopano, ndikhala ndikupitiliza nkhani zonse mwanthawi imodzi...

___GOLIDE___*P1*______Clarissa: Iwe Bertha, tawawone anyamata awo akudatsa apowo...Bertha: zamisala eti? anyamata ake at...
26/09/2017

___GOLIDE___
*P1*
______
Clarissa: Iwe Bertha, tawawone anyamata awo akudatsa apowo...
Bertha: zamisala eti? anyamata ake atiwo?
Clarissa: mmmmh abale mpaka zamisala? ndikunena awo avala ma worksuit amtundu wa mtambo anyamula nkhuni-wo.
Bertha: Ukunena avala zovala zopakika ndi oil akuwoloka msewu-wo?
Clarissa: Eya... Eya...
Bertha: Ndiye atani???
Clarissa: Hmmmm, basi zatha.
Bertha: Tiyeni tidzipita nthawi yatha.
Uku kudali kucheza kwa Clarissa ndi Bertha panthawi yankhomaliro wawo amene adakamuwonera pachiwaya cha tchipisi, pa Roundbout ya Kameza, Blantyre. Anyamata amene adali kulozeranawo ndinali ineyo (Jack) ndi mzanga Bless.
Ndipo nthawi imeneyi tinkachokera pa msika wina kumene timakagula nkhuni zophikira m'memo pa Garage pamene ndimaphunzirapo za Auto~Mechanic.
Clarissa ndi Bertha amaphunzira pa private secondary school inayake imene inayandikira pa Garage yathuyo.
Pamene Clarrisa ndi Bertha adachokapo pa chiwaya ankadya tchipisi paja, munjira yonse adali kukambirana...

25/07/2017

NTHAWI
*(P6)*
Anambewe atangochoka pamolopo, Martin adangozindikira munthu wina wamugwira kumboyo kwake.
Atangotembenuka anali odabwa kumuwona mtsikana amene ankatola nkhuni uja, anangofikira kumukumbatira, nthawi yomweyo nkuyamba kusinthana mate.
Malingana nkuti Martin anali akuchokera pa gule wina, anayesera kumukankha mtsikana uja kuti kuti asasewerenso. Ndipo panthawi imeneyo, mtsikanayo sadagonje, m'malo mwake adapitsa mkabudula mwa Martin kufuna kuiputa dala njoka imene idali ikumezera mate malinga nkuti idali ikuchokera pachitsime.
Mtsikanayu adayesetsa kuikankha kankha njokayi, koma nayo idachita mwano osadzuka pamene idagonapo. Atawona kuti sapindulapo kanthu mtsikanayu, adangomuwuza Martin kuti akumana madzulo, ndipo ngati zingalephereke akawulura kwa a Chosadziwa. Ndipo Martin adalephera kumuchondelera Mtsikanayo kuti atchule chinthu china chilichonse chimene akufuna kuti amulipire, koma kupatula masewera olumisana njokawo.
Mtsikanayu sanalore adawumilirabe kuti iye akufuna *******

Its Me your Admn,,,Sorry potenga nthawi yaitali osakupatsiran nkhani, Ntchito yandigwira pakhosi, but ndiziyesetsa kukul...
09/04/2017

Its Me your Admn,,,
Sorry potenga nthawi yaitali osakupatsiran nkhani, Ntchito yandigwira pakhosi, but ndiziyesetsa kukulemberani mpata ukapezeka.

Thanx...
for...
like this page!!!

14/03/2017

NTHAWI
*(P6)*
.....kodi anamukumbatira Martin anali ndini? dikirani *(P6)*

**Imeneyi ikufikani mukapanga like & comment *(P5)*
Ndiye mukangotero ndidziwa kuti tili limodzi, cozi kungotero kokha ndiye kuti mwandilipira ndikundipatsa chilimbikitso**

14/03/2017

NTHAWI
*(P5)*
Gule navinidwa ndithu mpaka Anambewe adayamba kumapepesa misonzi yosamba ikugwa, chifukwa adafikisidwa ku nyumba yeniyeni imene malemu gadafi amapezamo mpumulo.
Ndipo Anambewe amati akati ayesere kuvunitsa thupi kufuna kumugonjetsa Martin, amagonja adali iwowo. ndipo naye Martin adafika podziyiwala yekha kamba kakuti adayamba kuyikilapo mtima pa kaseweredwe kake kamene samafuna kuwoneka ngati kuti njoka yake inali yakufa, ndipo adawalumitsa nayo Anambewe mowilikiza.
Gule adaseweredwa ndithu kokwana kanayi, koma Anambewe ankangogonja okha chifukwa njoka ya Martin siyimagonja.
Zonse zitatha aliyese ankamuchitira manyazi mnzake, Anambewe anali ndi manyazi chifukwa anatulutsidwa misonzi ndi mwana wa chichepere. Nayenso Martin anali kuchita manyazi pogona ndi munthu woposa msinkhu wake.
Nthawi yobwerera kunyumba Anambewe adamuwuza Martin kuti aliyense ayendere yake kuwopa kugwidwa.
Ndipo atangochoka Anambewe, Martin adangozindikira munthu wina wamukumbatira kumbuyo kwake, ndipo atangotembenuk

Address

Mapazi Primary School, Post Office Box 150, Njuli
Blantyre
001

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when UNDER the Mlombwa TREE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category