Village Market Home

Village Market Home Village market home a home of quality kitchenware
(1)

Restocked !!!!! Wabwera original clear essence, thamangani akasi
11/06/2026

Restocked !!!!! Wabwera original clear essence, thamangani akasi

11/06/2026

Ma toy kuno ndiye ndi sankha wekha , mukapeza mpata mudzereko ku shop pa Clocktower mall or kameza petroda muzasilire, k...
11/06/2026

Ma toy kuno ndiye ndi sankha wekha , mukapeza mpata mudzereko ku shop pa Clocktower mall or kameza petroda muzasilire, kutali timatumiza 0888649419

11/06/2026

Kwacha bwanji kwanuko akasi, kuno kwacha bwino Jessie James kodi munatipanga kale follow? Tiyankhuleni ndi ku inbox lonjezo likwanilitsidwe mwai wakugwerani🔥🔥🔥🔥🔥🔥

08/06/2026

Munthu atakudalitsa ndi k100,000 ungapange nayo chani kuti nawenso after some months uzamudalitse wina ?

Kwabwera zodumphira misimisi 🤣🤣 kumadumpha kumeneko ngati jingo janga, village market kameza ndi Clocktower mall 0888649...
08/06/2026

Kwabwera zodumphira misimisi 🤣🤣 kumadumpha kumeneko ngati jingo janga, village market kameza ndi Clocktower mall 0888649419

Baby car seat available for K350,000. We are situated in Blantyre, at Clocktower Mall and Kameza Petroda Complex. Contac...
07/06/2026

Baby car seat available for K350,000. We are situated in Blantyre, at Clocktower Mall and Kameza Petroda Complex. Contact us at 0888649419.

04/06/2026

Village market ili ku Blantyre kwa kameza pa petroda filling station komanso pa Wenera pa Clocktower mall, kutali timatumiza 0888649419

Kwabwera ma colours enatu , aka utha kuika ma snacks or ma fruits k20,000 chimodzi , kutali timatumiza
04/06/2026

Kwabwera ma colours enatu , aka utha kuika ma snacks or ma fruits k20,000 chimodzi , kutali timatumiza

Chopangira juice ichi wa ma orange, mandimu, nanchesi ndi manyumwa, zangotsikiratu ku village market, ndiye simmene aboo...
03/06/2026

Chopangira juice ichi wa ma orange, mandimu, nanchesi ndi manyumwa, zangotsikiratu ku village market, ndiye simmene abookera ma nanchesi,shoooo

Address

Box 40469 Llz
Blantyre
00265

Opening Hours

Monday 07:00 - 19:30
Tuesday 07:00 - 19:30
Wednesday 07:00 - 19:30
Thursday 07:00 - 19:30
Friday 07:00 - 19:30
Saturday 07:00 - 19:30
Sunday 10:00 - 19:30

Telephone

+265888649419

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Village Market Home posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Village Market Home:

Shortcuts

Share