SASSO Chicken Farm

SASSO Chicken Farm We breed and supply dual purpose pure sasso chicks countrywide

28/08/2026
28/08/2026

MOMWE MUNGATHANILANE NDI MAVUTO AWA 👇KU NKHUKU ZANU

NJOKA ZA MIMBA / NYONGOLOSI
•Nyongolotsi za zitali zooneka zoyera zimapha nkhuku kwambiri. Nkhuku zimaonda
kwambiri ndipo zimatulutsa Chitosi(ndowe) zophatikizana ndi nyongolotsi.

ZOYENERA KUCHITA:
•Tikuyenera kuzipatsa mankhwala opha nyongolotsi a PIPERAZINE miyezi itatu iliyonse

KUTHANA NDI UTITILI/NTHATA
•Utitili umapha nkhuku kwambiri maka tianapiye. Tikuyenera kuti nthawi imene
nkhuku ikufungatila tiziwaza mankhwala otchedwa AKHERRI POWDER kapena ACTELLIC.

MATENDA A KAMWAZI (COCCIDIOSIS)
•Matendawa amachuluka mu khola momwe mumakhala chinyezi kwambiri ndipo nkhuku za msinkhu ulionse zimadwala. Matendawa amapha nkhuku koma ndi
ochizika.

ZIZINDIKIRO
• Kuzolikira pansi
• Chitosi chamadzimadzi chosakanikilana ndi magazi.
• Chilakolako cha kudya chimatha

KUPEWA KWAKE
• Mukhola muzikhala mouma nthawi zonse.
• Siyanitsani nkhuku zazikulu ndi zazing’ono.
• Zitosi zizichotsedwa pafupipafupo mkhola

That opportunity  has come again !
14/08/2026

That opportunity has come again !

Failry used 1240 eggs incubator for sale in Kasungu. Lets talk 0999274941
07/02/2026

Failry used 1240 eggs incubator for sale in Kasungu. Lets talk 0999274941

Incubator  for sale - 1240 egg capacityWe are selling a fully automatic 1240-egg-capacity incubator at a competitive pri...
07/02/2026

Incubator for sale - 1240 egg capacity

We are selling a fully automatic 1240-egg-capacity incubator at a competitive price of K1,500,000. It's a fairly used machine located at Kasungu boma .

For serious business, let's talk on 0999274941.

Powered by Sasso Chicken Farm

Sasso and kroilers chicks available. Lets talk on 0999274941/ 0888058957
12/01/2024

Sasso and kroilers chicks available. Lets talk on 0999274941/ 0888058957

Address

Riverside
Kasungu

Telephone

+265999274941

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when SASSO Chicken Farm posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to SASSO Chicken Farm:

Shortcuts

Share

Category