Nkhani ZA Abengo

Nkhani ZA Abengo CHOLINGA CHATHU:
1) KUPHUNZITSA
2) KUSANGALATSA
3) KUDZIWITSA

Ma Dollars aja ayambika
11/04/2025

Ma Dollars aja ayambika

Luso lamunthu uyuuu lidapita kuti??? Azungu atazindikika kuti munthuyu atha kupindulila dziko lamalawi adamutenga mkupit...
22/03/2025

Luso lamunthu uyuuu lidapita kuti??? Azungu atazindikika kuti munthuyu atha kupindulila dziko lamalawi adamutenga mkupita naye kunja kukamubela luso lija pobwela uko anangomupatsa chithumba cha ndlama lelo kuli ziiiiiiiii palibe chomwe akuchita!!!! Azungu mumatiphweteka ife anthu osauka

27/05/2022

Hala me 0999 698 249
If you whant to join NKHANI ZA BENGO whatsApp group

21/05/2022
10/05/2022

Pena ngati ndingokuwa kuti abingu mudafelanji?πŸ˜‚πŸ˜‚

10/05/2022

Mkadadziwa kuti sugar adzafika pa 2pin sibwezi mtakwatila!

26/03/2021

THAMBO LANGWA M'BANJA LATHU"
POMWE EMANUEL MZUMACHARO WATISIYA LELO MZIMU WALE UWUSE MU MTENDELE..

21/03/2021

Life is not easy, anthu ena anakula movutika ngati chigumu pansi moto ku mwamba moto. Moti sungawauze chochita

20/03/2021

*NKAZI ANANDIKANA UJA AMUPATSA MIMBA NAYE AMUKANANSO πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚ KOMA DZIKO LAPANSI PENA LIMAYENDAKO MUCHILUNGAMU*πŸ˜‚

😎

14/03/2021

What's on your *Kukwatiwa ndi sing'anja ndimavutodi bwanj*
Mayi: *amunanga madzi osamba ndayikako ku bath*.
Sing'anga: *Mizimu yakana ndisamba mawa* πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€?

10/03/2021

Mkazi anamangidwa zaka 10 pa mlandu oti anapha mwamuna wake. After kumaliza ukaidi wakewo, zinadziwika kuti mwamuna wake uja sanaphedwe koma anathawitsana ndi mkazi wina mkumakakhala kutali. Atafufuza komwe amakhala, anakapeza kuti ndizoonadi mwamunayo anali atakwatira mkazi wina. Chifukwa chopsa mtima, mkazi uja anaombera mwamunayo ndipo anafera pomwepo.
Fuso ndilakuti, *kodi mkaziyu akuyenera kumangidwaso kapena ayi?* fotokozani.. πŸ€·πŸ»β€β™‚οΈ

09/03/2021

*NDIKUDZIWA KUTI ADAKUTHAWANI NDIKUKUSIYANI NDI MWANA, MZOPWETEKA KWAMBIRI KOMA SANATHAWE NDI MADZI ZISAMBANI MUPEZA WINAπŸ˜†πŸ˜†πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ‘©β€β€οΈβ€πŸ‘¨*

Address

Kasungu

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhani ZA Abengo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category