Urban Lounge on MBC TV

Urban Lounge on MBC TV Best Entertainment platform in Malawi and Zambia this is a real program on MBC TV that brings you the latest and hottest videos from m-dubs

Kutsatira kupezeka kwa khanda lomwe linatayidwa m'dera la mfumu yaikulu Chidzuma m'boma la Kasungu, mayi wina waku Area ...
26/05/2026

Kutsatira kupezeka kwa khanda lomwe linatayidwa m'dera la mfumu yaikulu Chidzuma m'boma la Kasungu, mayi wina waku Area 36, mu mzinda wa Lilongwe, wati khandali ndi lake ponena kuti linachita kubedwa.

Mkulu woona za chisamaliro cha anthu m'bomali, a Ephraim Njikho, wati mayiyu anafikadi ku ofesi kwawo, koma kaamba koti palibe umboni wotsimikizika kuti khandali ndi lake, akana kupereka khandali.

Mmawu ake, wachiwiri kwa wofalitsa nkhani za apolisi m'bomali, a Miracle Hauli, watsimikiza za nkhaniyi ponena kuti ngakhale mayiyu anakakamila kufuna kutenga mwanayu komabe iye akufunsidwa kaye mafunso omwe athandizire kafukufuku opeza mwini wake wa khandali.

Full video ili mu comment 👇

Apolisi ku Salima atsimikiza kuti M'tsikana wa zaka 22, Olipa Wadzipha chifukwa mamuna yemwe analonjezana naye za banja ...
26/05/2026

Apolisi ku Salima atsimikiza kuti M'tsikana wa zaka 22, Olipa Wadzipha chifukwa mamuna yemwe analonjezana naye za banja wathetsa ubwenzi wawo.

Malingana ndi lipoti la polisi, M'tsikanayu anali pa ubwenzi wolonjezana banja ndi mamuna wina ndipo ali mkati mwa ubwenzi wawo Olipa anapezeka ndi pathupi(mimba) koma makolo ake a Olipa anamukakamiza Olipa kuchotsa pathupipo ndicholinga choti apitilize sukulu.

Bwenzi lake litaona kuti Olipa wachotsa pathupi linaganiza zothetsa ubwenzi wawo ndipo njondayi sinachedwe koma kupeza njole ina ya ponda apa nane ndipondepo.

Kamba kakuwawidwa mtima Olipa anagula mankhwala ophela makoswe ndi kumwa.

Video yomvesa chisoni kuonetsa thupi la Olipa likutengedwa ku Chipatala tayika mu comment 👇

Moomba aspirants join forces to boost support for Hichilema
06/05/2026

Moomba aspirants join forces to boost support for Hichilema

Police catch runaway Lusaka cop who stole k600,000 from bank(Full video in comments) A RUNAWAY Lusaka police officer who...
06/05/2026

Police catch runaway Lusaka cop who stole k600,000 from bank(Full video in comments)

A RUNAWAY Lusaka police officer who shocked many after grabbing himself a fat “retirement package” of K622,483 from Zanaco’s Civic Centre branch has finally been captured after months on the run.

The arrest brings to an end a real-life movie script that began with a daring daylight robbery by a man entrusted to protect the very money he stole.

Constable Emmanuel Mpatso Tembo, who had vanished into thin air after the heist, was yesterday cornered.

Police said the suspect had been moving like a shadow between Lusaka, the Copperbelt and Eastern Province, carefully dodging the long arm of the law.

Full video here👇👇
https://malawinazambia.blogspot.com/p/breaking-news-margin-0-padding-0-box_6.html

Residents of Nchelenge(Luapula province) were left shocked after an empty coffin was discovered by the roadside early th...
06/05/2026

Residents of Nchelenge(Luapula province) were left shocked after an empty coffin was discovered by the roadside early this morning.(Video check first comment)

According to reports, passersby came across a tightly closed and sealed coffin placed near the road. Alarmed by the unusual sight, they quickly informed the police.

Officers responded to the scene and opened the coffin, only to find that it was empty. However, two 50 Kwacha banknotes were found inside.

Full video is here👇👇👇
https://malawinazambia.blogspot.com/p/breaking-news-margin-0-padding-0-box_5.html

04/05/2026

Very sad, They want to kill her, Every plan has been revealed

Nkhuku yoweta sagula pa msika kakwatileni ku mudzi achimwene
04/05/2026

Nkhuku yoweta sagula pa msika kakwatileni ku mudzi achimwene

Ya lero
04/05/2026

Ya lero

Today, I choose to walk in quiet faith—trusting that even the smallest prayers are heard and every step is guided by God...
04/05/2026

Today, I choose to walk in quiet faith—trusting that even the smallest prayers are heard and every step is guided by God’s unseen hand. 🙏✨

04/05/2026

Good morning

🇲🇼 Malawi 3 - 0 RSA🇿🇦 Malawi Refuses to be bullied, Ngizwe Mchunu meets his match, Ali Kaka, a fearless and brave man al...
04/05/2026

🇲🇼 Malawi 3 - 0 RSA🇿🇦
Malawi Refuses to be bullied, Ngizwe Mchunu meets his match, Ali Kaka, a fearless and brave man all the way from Blantyre. (video in comments)

Ngizwe Mchunu : do you have papers?

Ali kaka: yes I have

Ngizwe Mchunu: so show me

Ali Kaka(replied with an attitude) :are you a police officer?

Ngizwe Mchunu : Yes am a police officer

Ali Kaka : Then show me your ID

Ngizwe Mchunu( realises it is about to go down) he starts barking like a dog, moving around like he wants to p*e then he tucks in his tail behind legs

It did not end well as the self acclaimed Giant was pushed and humiliated by 'Achimwene', Full video as he was being pushed 👇👇
Watch here👇👇
https://malawinazambia.blogspot.com/p/breaking-news-margin-0-padding-0-box_19.html

AKILA VERSION
Uyo wavala jersey ya green uyo, Ngizwe Mchunu, akumayenda ku Joni kumaopseza komaso kuthamangitsa anthu obwela(foreigners) ndiye anakumana ndi m'malawi olimba mtima otchedwa Ali Kaka, ndiye Ngizwe Mchunu waedzekedwa pakwawo

Onelani apa👇👇
Watch here👇👇
https://malawinazambia.blogspot.com/p/breaking-news-margin-0-padding-0-box_19.html

Address

Lilongwe Area 18

Telephone

+265888191464

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Urban Lounge on MBC TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share