16/07/2026
*How To minimize Losses during and after harvesting your pepper*
~ Do not pick un ripe peppers for drying! Osayerekeza kuthyola tsabola oti sanapsetsetse ngati mukufuna kukayanika
~ Musaike mu pepala la plastic tsabola osauma kwa nthawi yayitali
~ Chotsani ma stems poyanika
~ Yanikani pa thandala, mphasa, mkeka, lichelo koma osayanika pansi.. Pa ground ayi.
~ Onetsetsani kuti wawumitsitsa kwambiri tsabola wanu
*Wakutsina khutu ndi mnasi*