Bvimz de Bright

Bvimz de Bright Only God Knows What Is Happening

01/08/2023

Wang'omayoooo

25/07/2023

I remember it was 2018 pamene tidapita kukapanga ma interview a census cha kimalire kwa Dowa ndi lilongwe uko
Ndie titamaliza zonse amene ankapangisa ma interview adalephera kuulutsa zotsatra chifukwa kunali k*tada malo mwake adanena k*ti amene asqnkhidwe tiwayimbira phone potengera k*t mwatipatsa ma number anu kotero alitense akhare pa line kuchoka pano mpaka mawa madzulo
Nditafika kunyumba phone yanga idazima ndiye kudali ntchito kubweleka ma battery a phone kumakhara kusinthira even popita ku bathroom kuinyamura phone koma isadzalire
Mwamwayi tsiku lachiwili chakumadzulo ndipamene ndimaimbilidwa phone k*ti ndachita mwayi ndatengedwa nawo.
Tizikhara ndi chikhulupiliro nthawi zonse 🙏

13/06/2023

Apro

10/06/2023
28/01/2022

A friend in need is a friend indeed

09/07/2020

For the wages of sin it's death but the gift of God is enternal life

02/06/2020

To erra is Human

Address

Nsaru
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bvimz de Bright posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Bvimz de Bright:

Share