Kells Classic

Kells Classic Fascinators for hire Clutch bags for hire & sale
Ladies’ second-hand dresses

Area 49 Old Shire

0998 22

✨ Kels Classic – In One Place ✨

kells Classic in one placezikomo aka
09/09/2026

kells Classic in one place

zikomo aka

Aka ma bag awatu for sale Penatu hire imazatopetsa kkkkkk
09/09/2026

Aka ma bag awatu for sale Penatu hire imazatopetsa kkkkkk

kungoti wow wow wowone word for Aka
09/09/2026

kungoti wow wow wow

one word for Aka

💐THANK YOU, AKA! Lero tikufuna kungoti zikomo kwambiri, Aka, chifukwa cha support yanu yomwe mumatipatsa nthawi zonse. T...
09/09/2026

💐
THANK YOU, AKA!

Lero tikufuna kungoti zikomo kwambiri, Aka, chifukwa cha support yanu yomwe mumatipatsa nthawi zonse.

Timayamikira kwambiri chikondi chanu ndi momwe mumapitilira kutithandiza. Mulungu apitirize kukudalitsani kwambiri. 🙏🏽

Ndipo ukwati wina mukadzabwera, hire bag ndi yaulere — imeneyi ndi token yathu yaying’ono yoyamikira support yanu.

Zikomo kwambiri, Aka!
From all of us at Kells Classic — We Complete Your Look.

Azimai ulemu wanu mumakwana
08/09/2026

Azimai ulemu wanu mumakwana

Debuty parent naye kuionetsaZikomo aka for the support mumakwanaOne word for aka
08/09/2026

Debuty parent naye kuionetsa
Zikomo aka for the support mumakwana

One word for aka

Umakwana top fan we celebrate you Fascinator by us
07/09/2026

Umakwana top fan we celebrate you

Fascinator by us

Ndiwe dolo katatu umakwanaOne word for aka
07/09/2026

Ndiwe dolo katatu umakwana

One word for aka

Aka koma mwadzuka bwanji? weekend ifetu tinali ku shades of pink Kaya weekend yanu yayenda bwanji?Fascinator and bag by ...
07/09/2026

Aka koma mwadzuka bwanji? weekend ifetu tinali ku shades of pink Kaya weekend yanu yayenda bwanji?

Fascinator and bag by us
Kells Classic we complete your look

Aka zikomo chifukwa  cha support  yanuone word for akafascinator  and bag by uskells classic, we complete your look
05/09/2026

Aka zikomo chifukwa cha support yanu

one word for aka

fascinator and bag by us

kells classic, we complete your look

Address

Area 49 Old Shire
Lilongwe

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:30
Tuesday 08:00 - 17:30
Wednesday 08:00 - 17:30
Thursday 08:00 - 17:30
Friday 08:00 - 17:30
Saturday 08:00 - 17:30
Sunday 09:00 - 16:00

Telephone

+265996557572

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kells Classic posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Kells Classic:

Shortcuts

Share