25/09/2019
*CHIKONDI CHA MULAMU*
*part 1*
Story written by *fkiz nyimbiri*
ππππππΊπ«
"Iwe thocco zatenge ma key awa uwapelekeze mulamu ako akuvaya shopping"
Awa anali mawu a mchimwene wanga yemwe panthawiyi amakonzekera kupita ku meeting.
Ndinatenga ma key a galimoto ndinalowa kenako ndinayamba kudikilira mulamu abwere.
Zinatenga kanthawi paja muziwa akazi yawo ija akachoka kubafa aziphode kaye.
Ndili mgalimoto ndinazindikira kuti mkulu wanga amandipatsa galimoto chifukwa ndimayendetsa mosamala pa msewu,
Kenako ndinaona Mula akusegula chiseko analowa ndipo anakhara, galimoto inanyamuka koma thupi langa linasowa mtendele chifukwa Mula anavala ka siketi kakafupi ndipo ntchafu zonse zinali pa mtunda, ndimayendesa galimoto maso anga pasogolo chifukwa sindimafuna kuona ntchafu zopanda chilema,
Ndinazilankhulira mu mtima "kodi mkulu wanga akundipasilanji mayeselo otelewa pomulola mkazi wake kumavala tatifupi chonchi"?
Kenako tinafika pa shopping anagula zofuna zake kenako anakwera galimoto kuti tiuyambe ulendo wobwelera kunyumba, koma atangolowa anati
"Ukuziwa chani thocco*?
Ndinati "palibe"
Mwamuna wanga akupita ku America for 1 month ndinthawi zabwino bwanji.
Ndinamufusa "zabwino zimenezo kuti Mwamuna wanu akuchoka? Anayankha eya ndi nthawi Ya iwe ndi ine to enjoy.
Ndinayamba kudabwa ndimalankhulidwe ake ndipo ndimaona ngati she is joking, koma ndinazizwa akundiuza kuti ndiwapase kisi.
Ndinagwidwa ndi nthumazi,
Kenako anati tachangamuka iwe thocco kungokhara ngati sindiwe Mwamuna.
Zinandiwawa.
Ndinawafusa kodi ine ndi Mwamuna wanu mumamkonda ndani?
Anayankha mmaso muli gwaa "ndimakukonda iweyo"
Ndinamuuza mulamu ine zimenezo ayi.
Anayankha nati ufune usafune iwe ndiine tivina gule wakuchipinda, kenako anandigwira mokakamiza kuti ndiwapase kisi koma ndinakana ndipo ndinati ndimamulemekeza mkulu wanga I cannot do that.
Anayankha nati kodi pa centre Pali sign kuti ukafikapo iye azaziwa?
Ndinangoti kakasi kusowa chonena.
Ndinayasa galimoto ndinauyamba ulendo wobwelera tili mu njira mulamu anati ngati ukukana upeza mavuto kudyesa ndikudyese pano uzindikana, komaso ukakana kugonana ndikukhomelera ndikupasa mulandu uchoka pakhomo pano komaso ndimuuza Mwamuna wanga kuti umafuna kundigwililira,,,,,,,,,,,,
Ipitilirabe mu part 2
Ngati zilibwino ndifuna support yanu kuti ndipitilize kuponya
Thanks