DAPP Malawi Fundraising -Salima

DAPP Malawi Fundraising -Salima KULANDILA MA UPDATE OKHUZA DAPP SALIMA ZOMWE IMAPANGA DAILY

14/01/2023

Mwaswela bwanji ma customer nonse a DAPP Salima. mitengo yathu ya pa 15 January, 2023 ili motere :- Zovala, ma bedsheets, mattress covers, cartan's, ma bag, kid and ladies shoes ndi K 1800 while Men's shoes ndi K 3500

Happy hour timakhala nayo komaso timaonjezera zovala thawi ndi thawi

!!! Zikomo!!!

15/05/2022

Mwaswela bwanji ma customer nonse Dapp itsekulaso Katundu wina mawa
pa 16-05-22 thawi 07:30am.
shop ili pompaja pa Takumana moyang'anizana ndi msalura secondary school

14/04/2022

Date : 18. April 2022

14/04/2022

Hello our dear customer Tikukudziwitsani k*ti week ya mawa titsekulaso Katundu wa tsopano Monga zovala, Ma bag, ma blanket, ma Duvert, cartan ndi nsapato
Date. 18 April 202
thawi . 07:30am
malo Takumana opposite seventh day

20/02/2022

Mongokumbutsana makasitomala anthu mawa pa 21 -2-2022. tik*tsegula katundu watsopano Monga zovala, ma bag, sapato, ma Duvert, ma cartan ndi zina zambiri!! Thawi ndi 7:30 am malo Takumana opposite seventh day

Hello  our dear customer Tikukudziwitsani k*ti mawa pa  15 /11  /21  tik*tsekulaso katundu watsopano    katundu timatsek...
14/11/2021

Hello our dear customer
Tikukudziwitsani k*ti mawa pa 15 /11 /21 tik*tsekulaso katundu watsopano
katundu timatsekula pakadutsa ma week awiri !!!

Hello our dear customer   mwachimwemwe komasonso mwa nsangala tikukudziwitsan k*t mawa titsekulaso katundu wa tsopano Mo...
13/06/2021

Hello our dear customer mwachimwemwe komasonso mwa nsangala tikukudziwitsan k*t mawa titsekulaso katundu wa tsopano Monga ma Bag, zovala, ma blanket, ma duvet, nsapato. Mwa zina zomwe tilinazo nd zimenez

13/05/2021

Hello our dear customers its special announcement from DAPP SALIMA so that we wl have New Opening at this coming Monday which is 17/May/2021 things like Clothes, bags., Textile, Duvet, Blanket and shoes Come come!!!! opening time is 7:30Am up to 6:00pm ur almost welcome thanks. ..

This is for Tomorrow come our dear customers
04/04/2021

This is for Tomorrow come our dear customers

Mwa wina katundu amene tilinaye mawa ndi ameney
04/04/2021

Mwa wina katundu amene tilinaye mawa ndi ameney

04/04/2021

Mwachimwemwe komaso mwansangala ife a DAPP salima tikukudziwitsani k*ti mawa pa 5-04 - 2021 tik*tsekulaso katundu wa-new monga ma Bag, Zovala, zofunda ndI Nsapato DAPP ili patakuma moyang'anizana nd nsalula secondary school zafikeni timatsekula 7:30 Am k*tseka 6:00 pm timaonjezelaso zovala zina zikomo...

Today's price k 1300 about clothes and bags
28/03/2021

Today's price k 1300 about clothes and bags

Address

Dapp P. O Box 2732 Salima BT
Salima

Telephone

+265881542091

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DAPP Malawi Fundraising -Salima posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share