30/08/2026
Nkhani ya agogo athuwa itipatse Ife phunziro ngati tilidi ndi nzeru tikuyenera kulingalila bwino kufatsapo pamenepa.
Akuluakulu kunjaku kuli anthu ali ndi ndalama za nkhani nkhani ndipo kuchotsapo pa ndrama zawozo 5 million kwacha samamva kalikonse Koma akukanika kupanga Zimene Sheikh athuwa apanga. 🥺
Chabwino mulibe ma million Koma at least muli ndi Kuthekera kopanga China chake kuthandizira Deen ya Allāh yi.
Izi zitiphunzitse kudziyimira patokha tisamangodalira kumangodikirira Wina wake abwere nkutikankha lets be the first ones to help ourselves.
Izi zitiphunzitse kugwiritsa ntchito bwino zimene tili nazo ngakhale zikuoneka zochepa.
Izi zitiphunzitseso kuonetsa chidwi kudzikhuthura kwatunthu potukula Chipembedzo chokomachi. Komaso kuonetsa chidwi kuthandizana Wina ndi mnzake. etc...
I mean this is absolutely extra ordinary and amazing. ALLAH AKBAR ALLAH AKBAR ALLAH AKBAR ❤️🩹
Isn’t this beautiful? ❤️ May Allah accept it from him and make it a lasting charity (Sadaqah Jariyah)... ✍️