Let's Talk -Malawi Decides 2030

Let's Talk -Malawi Decides 2030 Under unofficial results

15/03/2026

Anthu inu akusamba mankhwala 🤣🤣🤣🤣🤣 He said this while laughing 🤣🤣🤣🤣

15/03/2026

❤️🦋:ine nazindikila conductor akundiuza k*t tilandire nawo kumufusa k*t mulandire nawo chan ati mai mwakweratu bus ya salima inu pano tili pa chezi😂🤣

15/03/2026

💔= ndinalila utsiku onse mpaka mai anga kundifunsa k*t kod ukudwala chani??? ndimvekele ndikubiba magazi😭😭😭

14/03/2026

Special enquiry ya Amaryllis Hotel ikuchita k*tiuza k*ti 100% umphawi waku Malawi ndi ochita kukhonza💔

12/03/2026

It's not easy having a child with irresponsible father, it's not easy paying the bills alone school fees, school stationary, hospital bills in short everything like bambowo anafa koma alimoyotu Aliso ndi ndalamazawo but I thank God zinandiphunzitsa kulimba mtima, kudaliraso mulungu komaso kudziwa kusaka ndalama single mothers shout power in jesus name, ndingokulimbikitsa single mom k*ti kukhala mayi sikulephera komaso no matter what olo zitumbuwa za nthochi gulisa chifukwa when the I love you fade the money in your pocket will stand still with you. I'm a proud mother because I choose to keep the baby though the world was against it today everybody is celebrating with me. Single moms shout Hallelujah

12/03/2026

Being divorced when my baby was 3 years yeah, at least my baby is 8 years turning 9 soon 🙏
Being a single mom it's not easy,ma ups and downs, sometimes we fail to give all the care for a child needy but I thank God for everything.Baby daddy ndy anaiwala kale kale sot Ali ndi mwana Loko moni ayii and it feels bad seeing your child not receiving the love from the father but the words of God says we have the good father who's God🙏
Yehova anapeleka ganyu ndipo we are surviving and making better plans next time I will have a home where I'll be taking care of ana amasiye ndi osiyidwawa pot ndinayamba kale k*telo @

Congratulations 🎉
10/03/2026

Congratulations 🎉

09/03/2026

Getting married after 30 is still beautiful, starting a family after 35 is still possible, buying your first house after 40 is still a boss move.

Don’t let people rush you with their timelines.

09/03/2026

Anandiuza k*ti mwana wawo ndiwa ng'ono sanafike popeleka mimba koma chonsecho wamkulu anali yeyo timasiyana dzaka ziwiri

09/03/2026

Ati waoyo ndi Mwana sangapereke mimba😅😅😅

09/03/2026

Anatiuza k*t mimba ndiyawo sangakane ndipo tipite tikakhale ku banja ifetu kupita kungokhala 1 day k*tacha wazapita kuntchito omweo osabwelelaso ife bas kumapasidwa chakudya ndi aneba after week tikudikilabe k*t mwina lelo abwela osabwelabe bas tinabwelelaso kwa amama mmmmmm ndipo Jona ine ayi dzikom until now sindimaziwaso k*t alik*t ndipo mwana wake sanamuonepo 8 years now my baby girl Abigail 🥰🥰🥰🥰 ndye anandiphunzisa kulimba mtima ndiso kulimbikila pano ndili ku Germany 🇩🇪 🤣

08/03/2026

Ineyo galimoto lot muli azibambo okhaokha sindikwera..bola Ali moyo, people are wicked

Address

Pretoria

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Let's Talk -Malawi Decides 2030 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share